Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 63
  • Ndife Mboni za Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Ndife Mboni za Yehova
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Ndife Mboni za Yehova!
    Imbirani Yehova
  • Ndife Mboni za Yehova!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Chuma Chapadera
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Chuma Chapadera
    Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 63

NYIMBO 63

Ndife Mboni za Yehova

Losindikizidwa

(Yesaya 43:​10-​12)

  1. 1. Amapanga milungu,

    Yehova samudziwa.

    Ndi Wamphamvuyonse,

    M’lungu woona.

    Milunguyo sidziwa

    Zomwe zili m’tsogolo.

    Milunguyo ilibe ntchito.

    M’lungu ndi Yehova yekha.

    (KOLASI)

    Mboni za Yehovafe

    Timalengeza konse.

    M’lungu wathu akalosera

    Zonse zimachitika.

  2. 2. Timalengeza dzina

    La Yehova Mulungu

    Ndi Ufumu wake

    Molimba mtima.

    Timathandiza ena

    Kudziwa choonadi.

    Akaphunzira amaimba

    Nyimbo yotamanda M’lungu.

    (KOLASI)

    Mboni za Yehovafe

    Timalengeza konse.

    M’lungu wathu akalosera

    Zonse zimachitika.

  3. 3. Ntchito yolalikira

    Za dzina la Yehova

    Imachenjezadi

    Olidetsawo.

    Imathandiza anthu

    Kukhululukidwadi.

    Imabweretsanso chimwemwe

    Komanso chiyembekezo.

    (KOLASI)

    Mboni za Yehovafe

    Timalengeza konse.

    M’lungu wathu akalosera

    Zonse zimachitika.

(Onaninso Yes. 37:19; 55:11; Ezek. 3:​19.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena