Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 69
  • Pitirizani Kulalikira za Ufumu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Pitirizani Kulalikira za Ufumu
  • Imbirani Yehova Mosangalala
  • Nkhani Yofanana
  • Pitani Patsogolo, Inu Atumiki a Ufumu!
    Imbirani Yehova
  • Patsogolo, Inu Aminisitala Aufumu!
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Pitani Patsogolo Mboninu!
    Imbirani Yehova
  • Pitani Patsogolo Mboninu
    Imbirani Yehova Mosangalala
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Mosangalala
sjj nyimbo 69

NYIMBO 69

Pitirizani Kulalikira za Ufumu

Losindikizidwa

(2 Timoteyo 4:5)

  1. 1. Pitani patsogolo ndithu

    Polalikira konse.

    Muthandize anthu ofatsa

    Kukonda choonadi.

    Ndi mwayidi kutumikira.

    Tizikonda ntchito yathu,

    Tizilalikira mwakhama

    Za dzina lake loyera.

    (KOLASI)

    Pitirizani kulalikira

    Padziko lonse.

    Pitirizani kukhala

    Okhulupirikabe.

  2. 2. Tonse tipite patsogolo,

    Abale ndi alongo,

    Odzozedwa ndi nkhosa zina,

    Tizilalikirabe.

    Anthu akufunika kuti

    Amve uthenga wabwino.

    M’lungu amatipatsa mphamvu

    Ndipo sitiopa kanthu.

    (KOLASI)

    Pitirizani kulalikira

    Padziko lonse.

    Pitirizani kukhala

    Okhulupirikabe.

(Onaninso Sal. 23:4; Mac. 4:​29, 31; 1 Pet. 2:21.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena