Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Otsatirawa:
Kodi lamulo lalikulu kwambiri ndi liti, nanga ndi lofunika bwanji? (Mat. 22:37, 38; Maliko 12:30)
Kodi tingapewe bwanji kukonda dziko? (1 Yoh. 2:15-17)
Kodi tingaphunzitse bwanji anthu ena kuti ‘azikonda dzina la Yehova’? (Yes. 56:6, 7)
Kodi tingasonyeze bwanji kuti timakonda abale athu mopanda chinyengo? (1 Yoh. 4:21)
Kodi makolo angaphunzitse bwanji ana awo kuti azikonda Yehova? (Deut. 6:4-9)
Kodi mungatani kuti Yehova akhale mnzanu wapamtima? (1 Yoh. 5:3)
Kodi tingatani kuti tisasiye kapena tiyambirenso kukonda Yehova? (Chiv. 2:4, 5)