BOKOSI 8B
Maulosi Atatu Okhudza Mesiya
1. “Amene Ali Woyenerera Mwalamulo” (Ezekieli 21:25-27)
NTHAWI ZA ANTHU AKUNJA (607 B.C.E.–1914 C.E.)
607 B.C.E.—Zedekiya anachotsedwa pa ufumu
1914 C.E.—Yesu amene ndi “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu komanso Mesiya anaikidwa kukhala Mfumu ndipo anakhala M’busa ndiponso Wolamulira
Bwererani ku mutu 8, ndime 12-15
2. “Mtumiki Wanga . . . Adzawadyetsa Komanso Adzakhala M’busa Wawo” (Ezekieli 34:22-24)
MASIKU OTSIRIZA (1914 C.E.–PAMBUYO PA ARAMAGEDO)
1914 C.E.—Yesu amene ndi “woyenerera mwalamulo” kukhala Mfumu komanso Mesiya anaikidwa kukhala Mfumu ndipo anakhala M’busa ndiponso Wolamulira
1919 C.E.—Kapolo wokhulupirika komanso wanzeru anasankhidwa kuti aziweta nkhosa za Mulungu
Akhristu odzozedwa okhulupirika anasonkhanitsidwa pamodzi ndi Mesiya yemwenso ndi Mfumu, ndipo kenako anakhala gulu limodzi ndi a khamu lalikulu
PAMBUYO PA ARAMAGEDO—Madalitso amene adzakhalepo Mfumu ikamadzalamulira adzakhalapo mpaka kalekale
Bwererani ku mutu 8, ndime 18-22
3. “Onsewo Adzalamuliridwa ndi Mfumu Imodzi” Mpaka Kalekale (Ezekieli 37:22, 24-28)