Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CA-brpgm21 tsamba 4
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2020-2021—Wokhala ndi Woimira Nthambi
  • Nkhani Yofanana
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2020-2021—Wokhala ndi Woyang’anira Dera
  • Chimwemwe Ndi Khalidwe Limene Mulungu Amapereka
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
    Pulogalamu ya Msonkhano Wadera Wokhala ndi Woimira Nthambi wa 2023-2024
  • Otanganidwa Koma Osangalala Potumikira Mulungu
    Nsanja ya Olonda—2009
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2020-2021—Wokhala ndi Woimira Nthambi
CA-brpgm21 tsamba 4

Mupeze Mayankho a Mafunso Awa:

  1. 1. Kodi ndi zinthu zitatu ziti zimene Yehova amatichitira kuti tizisangalala? (Sl 32:1-10)

  2. 2. Kodi tingatani kuti tizisangalala panopa? (Sl 5:11, 12; 91:14)

  3. 3. Kodi tingatani kuti tizisangalala pa utumiki wathu ngakhale kuti tikukumana ndi mavuto? (Mac 13:50-52; Aro 5:3-5)

  4. 4. Kodi tingatani kuti tipewe ‘kulemedwa’ n’kumakhala osasangalala? (Lu 21:34)

  5. 5. Kodi Yehova amatithandiza bwanji kuti tizikhala osangalala? (Sl 92:4, 5)

  6. 6. N’chiyani chingatithandize kuti tiziika Yehova patsogolo pathu nthawi zonse? (Aro 1:20; De 6:6-9; Afi 4:6; Sl 16:3)

© 2020 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena