Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • CO-pgm22 tsamba 8
  • Mawu kwa Osonkhana

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mawu kwa Osonkhana
  • Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
  • Nkhani Yofanana
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2021
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2020
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2023
  • Mawu kwa Osonkhana
    Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024
Onani Zambiri
Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2022
CO-pgm22 tsamba 8

Mawu kwa Osonkhana

Ubatizo Akulu amumpingo wanu akonza dongosolo labwino mogwirizana ndi mmene zinthu zilili m’dera lanu kuti anthu amene akufuna kubatizidwa, adzabatizidwe Loweruka chigawo cha m’mawa chikatha.

Zopereka Msonkhanowu wamasuliridwa m’zilankhulo zoposa 500. Ndalama zimene mumapereka mwa kufuna kwanu ndi zimene zimathandiza pa ntchitoyi yomwe ikuchitika padziko lonse. Mungapereke ndalama kudzera pa intaneti pogwiritsa ntchito donate.jw.org. Timayamikira kwambiri zopereka zanu, ndipo Bungwe Lolamulira likukuyamikirani chifukwa chothandiza ndi mtima wonse pa ntchito ya Ufumu.

Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu

Banja likuphunzira Baibulo ndi wachinyamata pogwiritsa ntchito buku lakuti “Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale”

Apainiya azaka zapakati pa 23 ndi 65 amene akufuna kuwonjezera utumiki wawo, akupemphedwa kuti auze mlembi wa mpingo wawo komanso alembe fomu ya pa intaneti yofunsira Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu.

Wakonzedwa ndi Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova

© 2022 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena