Penguins: By courtesy of John R. Peiniger
Lachisanu
“Chikondi n’choleza mtima” 1 Akorinto 13:4
M’Mawa
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 66 ndi Pemphero
9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: N’chifukwa Chiyani Tiyenera ‘Kukhala Oleza Mtima’? (Yakobo 5:7, 8; Akolose 1:9-11; 3:12)
10:10 NKHANI YOSIYIRANA: “Chilichonse Chili ndi Nthawi Yake”
• Muziganizira Mmene Yehova Amaonera Nthawi (Mlaliki 3:1-8, 11)
• Kulimbitsa Ubwenzi ndi Anzathu Kumatenga Nthawi (Miyambo 17:17)
• Kukula Mwauzimu Kumatenga Nthawi (Maliko 4:26-29)
• Kukwaniritsa Zolinga Kumatenga Nthawi (Mlaliki 11:4, 6)
11:05 Nyimbo Na. 143 ndi Zilengezo
11:15 KUWERENGA BAIBULO MWASEWERO: Davide Anayembekezera Yehova (1 Samueli 24:2-15; 25:1-35; 26:2-12; Salimo 37:1-7)
11:45 Muzisangalala ndi Kuleza Mtima kwa Mulungu (Aroma 2:4, 6, 7; 2 Petulo 3:8, 9; Chivumbulutso 11:18)
12:15 Nyimbo Na. 147 ndi Kupuma
Masana
1:35 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
1:45 Nyimbo Na. 17
1:50 Muzitsanzira Kuleza Mtima kwa Yesu (Aheberi 12:2, 3)
2:10 NKHANI YOSIYIRANA: Muzitsanzira Anthu Amene Anadalitsidwa Chifukwa cha Kuleza Mtima
• Abulahamu ndi Sara (Aheberi 6:12)
• Yosefe (Genesis 39:7-9)
• Yobu (Yakobo 5:11)
• Moredekai ndi Esitere (Esitere 4:11-16)
• Zekariya ndi Elizabeti (Luka 1:6, 7)
• Paulo (Machitidwe 14:21, 22)
3:10 Nyimbo Na. 11 ndi Zilengezo
3:20 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Chilengedwe Chimatiphunzitsa Zokhudza Mmene Yehova Amaonera Nthawi
• Zomera (Mateyu 24:32, 33)
• Zolengedwa za M’madzi (2 Akorinto 6:2)
• Mbalame (Yeremiya 8:7)
• Tizilombo (Miyambo 6:6-8; 1 Akorinto 9:26)
• Nyama Zapamtunda (Mlaliki 4:6; Afilipi 1:9, 10)
4:20 “Simukudziwa Tsiku Kapena Ola Lake” (Mateyu 24:36; 25:13, 46)
4:55 Nyimbo Na. 27 ndi Pemphero Lomaliza