Kodi Mulungu woona ndi ndani?
“Yehova ndi Mulungu woonadi. Iye ndi Mulungu wamoyo.”—Yeremiya 10:10.
Ganizirani izi
Mulungu ali ndi dzina.—Salimo 83:18.
Iye amalankhulana ndi anthu.—2 Timoteyo 3:16, 17.
Iye amafuna kutithandiza.—Salimo 145:18, 19.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania