CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 MBIRI 29-32
Tizichita Khama Polambira Yehova
Losindikizidwa
Hezekiya anathandiza anthu kuti ayambenso kulambira Yehova
746-716 B.C.E.
Hezekiya Analamulira Kuyambira mu
NISANI 746 B.C.E.
Tsiku loyamba mpaka la 8: Anayeretsa Bwalo la Mkati
Tsiku la 9 mpaka la 16: Anayeretsa Nyumba ya Yehova
Anapereka nsembe yophimba machimo a Aisiraeli onse ndipo anthu anayambanso kulambira Mulungu
740 B.C.E.
Mzinda wa Samariya Unawonongedwa
Hezekiya anasonkhanitsa anthu kuti alambire Yehova
Anthu anatumidwa kukapereka makalata olengeza za Pasika. Anapereka makalatawa kuyambira ku Beere-seba mpaka ku Dani
Ena ananyozera uthengawo koma ena anamvera