CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 26-33
Tizidalira Yehova Kuti Tikhale Olimba Mtima
Davide analimba mtima chifukwa chokumbukira mmene Yehova anamupulumutsira
Yehova anapulumutsa Davide kwa mkango
Yehova anathandiza Davide kupha chimbalangondo kuti ateteze nkhosa
Yehova anathandiza Davide kupha Goliyati
Kodi n’chiyani chingatithandize kukhala olimba mtima ngati Davide?
Pemphero
Kulalikira
Kupezeka pamisonkhano
Kuphunzira Baibulo patokha komanso kulambira kwa pabanja
Kulimbikitsa ena
Kukumbukira mmene Yehova anatithandizira nthawi ina m’mbuyomu