Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsamba 7
  • Kodi Munthu Wofunika Kwambiri pa Moyo Wanu ndi Ndani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Munthu Wofunika Kwambiri pa Moyo Wanu ndi Ndani?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Mmene Yehova Akuyankhira Pemphero Lochokera Pansi Pamtima
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Chigawo 2
    Mverani Mulungu
  • Kulemera Kungayese Chikhulupiriro Chanu
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Mfundo Zazikulu za Chigawo Chachitatu ndi Chachinayi cha Masalmo
    Nsanja ya Olonda—2006
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 July tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MASALIMO 79-86

Kodi Munthu Wofunika Kwambiri pa Moyo Wanu ndi Ndani?

Munthu akuimba zeze

Munthu amene analemba Salimo 83 ayenera kuti anali mdzukulu wa Asafu, yemwe anakhalapo pa nthawi imene Mfumu Davide anali ndi moyo. Salimo limeneli linalembedwa pa nthawi imene atumiki a Yehova ankaopsezedwa ndi mitundu ina.

83:1-5, 16

  • Amene analemba Salimo limeneli anatchula kwambiri za dzina la Mulungu komanso ulamuliro wake m’malo moganizira kwambiri za moyo wake womwe unali pangozi

  • Masiku anonso atumiki a Mulungufe timaopsezedwa ndi anthu ena. Koma tikamakhalabe okhulupirika, dzina la Yehova limalemekezedwa

83:18

  • Yehova amafuna kuti tidziwe dzina lake

  • Zochita zathu ziyenera kumasonyeza kuti timaona Yehova kukhala wofunika kwambiri pa moyo wathu

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena