Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsamba 7
  • “Phunzitsa Mwana M’njira Yomuyenerera”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Phunzitsa Mwana M’njira Yomuyenerera”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Kumvetsa Cholinga cha Kulanga
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Makolo Phunzitsani Ana Anu Mwachikondi
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Kodi Mungatani Kuti Muzilangiza Bwino Ana Anu?
    Nsanja ya Olonda—2014
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 October tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MIYAMBO 22-26

“Phunzitsa Mwana M’njira Yomuyenerera”

Mayi akuwerenga mpukutu ndi mwana wawo wamkazi ndipo bambo akuumba ziwiya ndi mwana wawo wamwamuna

Buku la Miyambo lili ndi malangizo abwino amene angathandize makolo. Mofanana ndi mfundo yakuti kuwongola mtengo n’kulinga uli waung’ono, tikamaphunzitsa bwino ana nthawi zambiri amapitiriza kutumikira Yehova akakula.

22:6

  • Munthu akumangirira kamtengo kuti kakule bwino

    Kuphunzitsa bwino ana kumafuna nthawi yambiri komanso khama

  • Makolo ayenera kukhala chitsanzo chabwino ndipo ayenera kuphunzitsa, kulangiza, kulimbikitsa ndiponso nthawi zina kupereka chilango kwa ana awo

22:15

  • Mawu amene anawamasulira kuti ‘kulanga’ mulembali amatanthauzanso kuphunzitsa ndiponso kulangiza mwana mwachikondi n’cholinga choti asinthe maganizo ndiponso mtima wake

  • Ana amafunika kulangizidwa m’njira zosiyanasiyana

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena