Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 March tsamba 6
  • Muzithandiza Banja Lanu Kuti Lizikumbukira Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzithandiza Banja Lanu Kuti Lizikumbukira Yehova
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Mphatso Yothandiza kwa Mabanja
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2011
  • Kulambira kwa Pabanja Kuzikhala Kosangalatsa
    Nsanja ya Olonda—2014
  • “Mawu Awa . . . Azikhala Pamtima Pako”
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Muzilambira Yehova Mogwirizana
    Banja Lanu Likhoza Kukhala Losangalala
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 March tsamba 6

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzithandiza Banja Lanu Kuti Lizikumbukira Yehova

Yeremiya anapatsidwa ntchito yochenjeza Ayuda kuti adzawonongedwa chifukwa chakuti anaiwala Mulungu wawo Yehova. (Yer. 13:25) Kodi n’chiyani chinachititsa kuti zinthu zifike poipa chonchi ku Yuda? Mabanja achiisiraeli anali atasiya kukonda Yehova. Zikuoneka kuti amuna amene anali ndi banja sankatsatira malangizo amene Yehova anapereka pa Deuteronomo 6:5-7.

Mayi amene akulera yekha ana akusangalala ndi ana ake pochita Kulambira kwa Pabanja; banja likugwiritsa mapu a malo otchulidwa m’Baibulo pa Kulambira kwa Pabanja

Masiku ano mabanja amene amakonda kwambiri Yehova amathandiza kuti zinthu ziziyenda bwino mumpingo. Amuna angathandize anthu a m’banja lawo kuti azikumbukira Yehova pochita nawo Kulambira kwa Pabanja nthawi zonse komanso m’njira yabwino. (Sal. 22:27) Pambuyo poonetsa vidiyo yakuti “Mawu Awa . . . Azikhala Pamtima Pako”​—Kucheza ndi Mabanja, kambiranani mafunso awa:

  • Kodi mabanja ena athana bwanji ndi mavuto amene ambiri amakumana nawo pochita Kulambira kwa Pabanja?

  • Kodi timapindula bwanji tikamachita Kulambira kwa Pabanja nthawi zonse komanso m’njira yabwino?

  • Kodi ndi mavuto ati amene mumakumana nawo okhudza Kulambira kwa Pabanja, nanga mungawathetse bwanji?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena