Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 April tsamba 3
  • Muzilola Kuti Yehova Aziumba Maganizo ndi Makhalidwe Anu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muzilola Kuti Yehova Aziumba Maganizo ndi Makhalidwe Anu
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Tiziyamikira Kuti Yehova Amatiumba
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Lolani Kuti Yehova Azikuumbani Ndi Malangizo Ake
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Kodi Mumalola Kuti Yehova Azikuumbani?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Kodi Ndani Amaumba Maganizo Anu?
    Nsanja ya Olonda—1999
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 April tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YEREMIYA 17-21

Muzilola Kuti Yehova Aziumba Maganizo ndi Makhalidwe Anu

Munthu akuumba chinthu

Muzivomereza ndi mtima wonse kuti Yehova akuumbeni

18:1-11

  • Yehova amatiumba pogwiritsa ntchito malangizo kapena uphungu

  • Tiyenera kukhala oumbika komanso omvera

  • Yehova satikakamiza kuchita zinthu zimene sitikufuna

Woumba amatha kuchita zimene akufuna ndi chinthu chimene akuumbacho

  • Popeza Yehova anatipatsa ufulu wosankha zochita, tingasankhe kuvomereza kuti azitiumba kapena kukana

  • Yehova amachita zinthu ndi anthu mogwirizana ndi mmene anthuwo akutsatirira malangizo ake

    M’bale akusiya kukambirana ndi akulu kenako akusintha maganizo n’kubwereranso, ndipo izi zikusonyeza zimene zimachitika Woumba Wamkulu akamatiumba

Kodi ndikufuna kuti Yehova andiumbe m’njira ziti?

KODI MUKUDZIWA?

Zidutswa zili pambali pa mtsuko

Kale anthu ankagwiritsa ntchito kwambiri dongo popanga zinthu. Dongo likakhala lofewa silivuta kuumba ndipo zimene zingalembedwe padongo loteroli sizifufutika. Komabe chinthu chopangidwa ndi dongo sichikhala cholimba kwenikweni ngakhale chitaotchedwa pamoto.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena