CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 39-41
Mmene Masomphenya a Ezekieli Onena za Kachisi Akutikhudzira
Zipinda za alonda komanso zipilala zimatithandiza kudziwa kuti Yehova ali ndi mfundo zapamwamba za makhalidwe abwino zokhudza kulambira koyera
Dzifunseni kuti, ‘Kodi ndingasonyeze m’njira ziti kuti ndimatsatira mfundo zapamwamba komanso zolungama za Yehova?’