Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 September tsamba 4
  • Aisiraeli Omwe Anachoka ku Ukapolo Analandira Madalitso

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Aisiraeli Omwe Anachoka ku Ukapolo Analandira Madalitso
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Ika Mtima Wako pa’ Kachisi wa Mulungu!
    Nsanja ya Olonda—1999
  • ‘Mugawane Dzikoli Kuti Likhale Cholowa Chanu’
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • “Ili ndi Lamulo Lokhudza Kachisi”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • ‘Ufotokoze za Kachisiyu’
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 September tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 46-48

Aisiraeli Omwe Anachoka ku Ukapolo Analandira Madalitso

Masomphenya a Ezekieli onena za kachisi analimbitsa mitima ya Aisiraeli omwe anali ku ukapolo ndipo anatsimikiza kuti maulosi onena zoti adzabwerera kwawo adzakwaniritsidwa. Anthu amene Yehova anawadalitsa ankaona kuti kulambira koyera n’kofunika kwambiri.

Aisiraeli omwe anachoka ku ukapolo anasangalala ndi dziko lomwe munali zakudya zochuluka

Masomphenyawa anasonyeza kuti Aisiraeli azidzachita zinthu mwadongosolo, mogwirizana komanso adzakhala otetezeka

47:7-14

  • Dziko labwino lokhala ndi zakudya zochuluka

  • Banja lililonse linali ndi cholowa

Malo asanagawidwe kwa anthu, anaika padera gawo lina la malowo monga “chopereka” kwa Yehova

48:9, 10

Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimaika kulambira Yehova pamalo oyamba? (w06 4/15 27-28 ¶13-14)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena