Paulo ndi Baranaba ali kwa Serigio Paulo
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 12-14
Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri
Baranaba ndi Paulo anagwira ntchito mwakhama pothandiza anthu kuti akhale Akhristu ngakhale kuti ankatsutsidwa kwambiri
Ankalalikira anthu a mitundu yosiyanasiyana
Ankalimbikitsa ophunzira atsopano kuti “akhalebe m’chikhulupiriro”