Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsamba 4
  • “Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Dipo Ndi ‘Mphatso Yangwiro’ Yochokera kwa Atate
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Dipo la Yesu Ndi Mphatso ya Mulungu Yamtengo Wapatali Kuposa Zonse
    Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?
  • Dipo la Yesu Ndi Mphatso Yamtengo Wapatali Imene Mulungu Anatipatsa
    Zimene Baibulo Limaphunzitsa
  • Tiziyamikira Mphatso ya Dipo
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 February tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 4-6

“Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake Kwa Ife”

5:8, 18, 21

Nsembe ya dipo ya Yesu imathandiza kumvetsa nkhani zofunika kwambiri monga ya kuyeretsedwa kwa dzina la Mulungu komanso kudziwa kuti Yehova yekha ndiye woyenera kulamulira. Nsembeyi imathandizanso kuti Yehova azitiona kuti ndife olungama ndiponso kuti tidzapeze moyo wosatha umene adzapereke kwa anthu omvera.

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira nsembe ya dipo?

  • Munthu akubatizidwa

    Kudzipereka komanso kubatizidwa kumasonyeza kuti ndife okhulupirika ndipo tikufuna kukhala anthu a Yehova

  • Abale awiri akulalikira uthenga wabwino

    Tikamalalikira uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu timasonyeza kuti timatsanzira Yehova pankhani yokonda anthu amitundu yonse.​—Mat. 22:39; Yoh. 3:16

Kodi ndingasonyeze m’njira zinanso ziti kuti ndimayamikira nsembe ya dipo imene Yehova anapereka?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena