Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 March tsamba 4
  • Kodi Ndinu Munthu Wakuthupi Kapena Munthu Wauzimu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Ndinu Munthu Wakuthupi Kapena Munthu Wauzimu?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Munthu Wauzimu Ndi Wotani? Kodi Ndingakhale Munthu Wauzimu Popanda Kukhala M’chipembedzo Chilichonse?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
  • Kodi Munthu Wauzimu Ndi Wotani?
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Pitirizani Kukula Mwauzimu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
  • Banja Lachikristu Limaika Zinthu Zauzimu Poyamba
    Nsanja ya Olonda—1993
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 March tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 AKORINTO 1-3

Kodi Ndinu Munthu Wakuthupi Kapena Munthu Wauzimu?

2:14-16

Aliyense ayenera kupitirizabe kukula mwauzimu n’kufika pomaona zinthu mmene Yehova amazionera. (Aef. 4:23, 24) Kuti zimenezi zitheke tiyenera kumaphunzira Mawu a Mulungu, kukhala ndi zolinga zauzimu komanso kuyesetsa kukhala ndi makhalidwe amene mzimu woyera umatulutsa.

Zosangalatsa, zolinga komanso anthu amene munthu wakuthupi komanso wauzimu amacheza nawo

Kodi ubwenzi wanu ndi Yehova wakula bwanji panopa mukayerekezera ndi mmene unalili chaka chapitachi, zaka 10 zapitazo kapena mutangobatizidwa kumene?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena