Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 June tsamba 5
  • “Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • ‘Tavalani Zida Zonse za Mulungu’
    Nsanja ya Olonda—1992
  • “Tavalani Zida Zonse za Mulungu”
    Nsanja ya Olonda—2004
  • Mmene Mungadziŵire ndi Kuthetsera Chofooka Chilichonse Chauzimu
    Nsanja ya Olonda—1999
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 June tsamba 5
Munthu wavala zida zonse zankhondo

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AEFESO 4-6

“Valani Zida Zonse Zankhondo Zochokera kwa Mulungu”

6:11-17

Mtumwi Paulo anayerekezera Akhristu ndi asilikali omwe akumenya nkhondo. Adani athu ndi “makamu a mizimu yoipa.” Ngakhale timaoneka ofooka komanso osatetezeka, tingapambane nkhondoyi ngati titavala “zida zonse zankhondo zochokera kwa Mulungu.”

Tchulani dzina la chida chilichonse komanso zimene chikutanthauza

Chida chankhondo chilichonse

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi ndimavala zida zonse zankhondo?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena