Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 October tsamba 3
  • “Khalani Oyera”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Khalani Oyera”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Atumiki a Mulungu Ayenera Kukhala Oyera
    Kodi Mulungu Amafunanji kwa Ife?
  • ‘Muzikumbukira Kukhalapo kwa Tsiku la Yehova’
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Mulungu Amakonda Anthu Oyera
    Kodi Mungatani Kuti ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’?
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 October tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1 PETULO 1-2

“Khalani Oyera”

1:14-16

Tiyenera kukhala oyera, kapena kuti aukhondo kuti Yehova azisangalala ndi kulambira kwathu. Kodi timakhala bwanji oyera . . .

  • M’bale wachinyamata wakonzeka kuti azipita kumisonkhano koma bambo ake omwe si Amboni akumukalipira

    mwauzimu?

  • Mwamuna ndi mkazi wake akufufuza pagulu la mafilimu achiwerewere, oonetsa zachiwawa komanso azamatsenga kuti apeze filimu yomwe angaonere

    mwamakhalidwe?

  • Mzimayi akutsuka poto

    mwakuthupi

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena