Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsamba 6
  • Yakobo Anakwatira

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yakobo Anakwatira
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Moyo Wawo Unali Wovuta Koma “Anamanga Nyumba ya Isiraeli”
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Yakobo Anaona Zinthu Zauzimu Kukhala Zofunika
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Yakobo ali ndi Banja Lalikulu
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Yakobo Amka ku Harana
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 March tsamba 6

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 29-30

Yakobo Anakwatira

29:18-28

Mwamuna ndi mkazi wake akukambirana, agwirana manja komanso akhala moyandikana. Pambali pawo pali Baibulo lotsegula.

Yakobo sankadziwa kuti akumana ndi zotani pamene ankakwatira. Akazi ake, Rakele ndi Leya anayamba kulimbana. (Ge 29:32; 30:1, 8) Ngakhale m’banja lake munali mavuto, Yakobo ankaonabe kuti Yehova akumuthandiza. (Ge 30:29, 30, 43) M’kupita kwa nthawi ana ake anadzakhala mtundu wa Isiraeli.​—Ru 4:11.

Masiku ano, anthu omwe asankha kukwatira angakumanenso ndi mavuto. (1Ak 7:28) Komabe akhoza kukhala ndi banja labwino komanso losangalala ngati amadalira Yehova ndiponso kutsatira mfundo za m’Baibulo.​—Miy 3:5, 6; Aef 5:33.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena