Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 October tsamba 2
  • Thawani Kulambira Mafano

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Thawani Kulambira Mafano
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Nkupeŵeranji Kulambira Mafano?
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Tingatani Kuti Mulungu Azisangalala Ndi Kulambira Kwathu?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
  • Peŵani Kulambira Mafano Kwamtundu Uliwonse
    Nsanja ya Olonda—1993
  • Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 October tsamba 2
Aisiraeli akuvina mozungulira mwana wa ng’ombe wagolide.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 31-32

Thawani Kulambira Mafano

32:1, 4-6, 9, 10

Zikuoneka kuti Aisiraeli anatengera maganizo a Aiguputo pa nkhani yolambira mafano. Masiku ano, anthu angalambire mafano m’njira zosiyanasiyana ndipo njira zina zingakhale zovuta kuzizindikira. Ngakhale kuti sitingalambire mafano enieni, tikhoza kuchita zimenezi tikamalola zinthu zimene timalakalaka kutilepheretsa kulambira Yehova ndi mtima wonse.

Anthu a m’banja limodzi akuchita zinthu za tsiku ndi tsiku. 1. Bambo yemwe ndi kalipentala akugwira ovataimu. 2. Mwana akusewera magemu apakompyuta. 3. Mayi akugula zinthu kushopu yapamwamba.

Kodi ndi zinthu ziti zimene ndimachita tsiku ndi tsiku zomwe zingandisokoneze polambira Yehova, nanga ndingapewe bwanji zimenezi?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena