Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 6
  • Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Madyerero Osaiŵalika a m’Mbiri ya Israyeli
    Nsanja ya Olonda—1998
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 6
Banja la Chiisiraeli likumanga msasa padenga la nyumba mosangalala. Abale akupatsana moni komanso kulandirana m’Nyumba ya Ufumu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zikondwerero Zomwe Zimatikhudza

Pasika komanso Chikondwerero cha Mikate Yopanda Chofufumitsa (Le 23:​5, 6; it-1 826-​827)

Chikondwerero cha Masabata (Pentekosite) (Le 23:​15, 16; it-2 598 ¶2)

Chikondwerero cha Misasa (Le 23:34; w14 5/15 28 ¶11)

Tikhoza ‘kumakhala osangalala’ tikamaganizira kwambiri tanthauzo la zikondwerero zimene Ayuda ankachita komanso mmene Yehova adzakwaniritsire malonjezo ake.​—De 16:15.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena