Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsamba 14
  • Utumiki wa Alevi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Utumiki wa Alevi
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Kulambira kwa Pakachisi Kunali kwa Dongosolo
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Chilamulo Chinkasonyeza Bwanji Kuti Yehova Amaganizira Anthu Osauka?
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • “Ine Ndine . . . Cholowa Chako”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Ndi Cholowa Changa
    Nsanja ya Olonda—2011
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 January tsamba 14
Alevi akugwira ntchito zawo. 1. Mlevi akuthira madzi m’beseni la mkuwa. 2. Mlevi akukoka ngolo yomwe muli mitsuko yadothi. 3. Mlevi wanyamula mtsuko wadothi paphewa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Utumiki wa Alevi

Yehova anatenga Alevi m’malo mwa ana aamuna oyamba kubadwa a Aisiraeli (Nu 3:​11-13; it-2 683 ¶3)

Alevi anali ndi mwayi wochita utumiki wapadera kwambiri (Nu 3:​25, 26, 31, 36, 37; it-2 241)

Alevi ankagwira ntchito zawo zonse akakhala ndi zaka zapakati pa 30 ndi 50 (Nu 4:​46-48; it-2 241)

Alevi aamuna a m’banja la Aroni ankagwira ntchito zaunsembe. Alevi ena onse aamuna ankangowathandiza. N’chimodzimodzinso mumpingo wa Chikhristu masiku ano. Abale ena audindo amasamalira maudindo akuluakulu, pamene ena amagwira ntchito zina ndi zina.

M’bale wachinyamata akuyang’ana mosamala kwambiri fomu yoitanitsira mabuku. M’bale wachikulire akuyang’ana zimene akuchitazo ndipo akumwetulira.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena