Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsamba 14
  • Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Yehova Amatsogolera Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • “Ine Ndine . . . Cholowa Chako”
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amasintha Temberero N’kukhala Dalitso
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Mmene Chikhulupiriro Chimatithandizira Kukhala Olimba Mtima
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 March tsamba 14

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kodi Zochita za Munthu Mmodzi Zingasinthe Zinthu?

Aisiraeli anayamba kuchita zoipa chifukwa chokopedwa ndi Amowabu (Nu 25:1, 2; lvs 118 ¶1-2)

Kusakhulupirika komanso kudzikonda kwa Aisiraeli kunakwiyitsa Yehova (Nu 25:3-5; lvs 119 ¶4)

Yehova anabweza mkwiyo wake chifukwa cha munthu mmodzi amene anachita zinthu molimba mtima (Nu 25:6-11)

Mtsikana wa Mboni akugwiritsa ntchito kabuku kakuti ‘Mmene Moyo Unayambira’ popereka lipoti kwa anzake m’kalasi. Mtsikana wina akuimika mkono.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Kodi ndi pa zochitika ziti pamene ndingafunike kulimba mtima n’kuchita zinthu zosiyana ndi ena?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena