Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 10
  • “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • “Lupanga la Yehova ndi la Gideoni”
    Nsanja ya Olonda—2005
  • Zimene Akulu Angaphunzire pa Chitsanzo cha Gidiyoni
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
  • Gideon ndi Amuna Ake 300
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
  • Kudzichepetsa N’kwabwino Osati Kunyada
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 10
Gidiyoni ndi amuna amene ali nawo akufuula atanyamula zounikira komanso malipenga.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Pita ndi Mphamvu Zimene Ndakupatsazi”

Yehova anapatsa Gidiyoni utumiki wovuta (Owe 6:2-6, 14)

Gidiyoni ankadziona kuti ndi wosayenerera (Owe 6:15; w02 2/15 6-7)

Gidiyoni anakwanitsa kuchita utumikiwu chifukwa cha mphamvu za Yehova (Owe 7:19-22; w05 7/15 16 ¶4)

Abale awiri ali mu utumiki ndipo akufika pakhomo la mzimayi. M’bale wina ali panjinga ya olumala ndipo m’bale winayo akumukankha.

Yehova amayembekezera kuti tizigwiritsa ntchito mphamvu zathu pomulambira. Mzimu wake woyera ungatithandize pamene tafooka komanso kukwanitsa zomwe sitikanatha kuchita.​—Yes 40:30, 31.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena