Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsamba 13
  • Yefita Anali Munthu Wauzimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yefita Anali Munthu Wauzimu
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Nkhani Yofanana
  • Anasangalatsa Bambo Ake Komanso Yehova
    Phunzitsani Ana Anu
  • Yehova Amadalitsa Anthu Okhulupirika
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • Yefita Anasunga Chowinda Chake kwa Yehova
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Ankakondedwa Ndi Mulungu Komanso Anzake
    Nsanja ya Olonda—2011
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
mwb21 November tsamba 13

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yefita Anali Munthu Wauzimu

Yefita sanasungire ena zifukwa (Owe 11:5-9; w16.04 7 ¶9)

Yefita ankaphunzira zimene Yehova ankachita ndi anthu ake (Owe 11:12-15; it-2 27 ¶2)

Yefita ankaganizira nkhani yofunika kwambiri yakuti Yehova ndiye Mulungu woona (Owe 11:23, 24, 27; it-2 27 ¶3)

Zithunzi: 1. M’bale akuwerenga Baibulo. 2. M’bale akulankhulana mwachikondi ndi mkazi wake. 3. M’bale ndi mkazi wake akhala pansi mwaulemu pamene anthu ena aimirira kuti achitire sailuti mbendera.

Kodi ndi zinthu ziti zimene ndimachita zomwe zimasonyeza kuti ndine munthu wauzimu?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena