Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsamba 5
  • Chilengedwe Chimatithandiza Kuti Tizidalira Kwambiri Nzeru za Yehova

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chilengedwe Chimatithandiza Kuti Tizidalira Kwambiri Nzeru za Yehova
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Mmene Nyerere Zimapewera Kutchingirana Njira
    Kodi Zinangochitika Zokha?
  • Nyerere Zalusa!
    Galamukani!—2003
  • “Pita ku Nyerere”
    Galamukani!—1990
  • Tizilombo Tochotsa Nyansi Mogometsa
    Galamukani!—2002
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 January tsamba 5
Zithunzi: 1. Nyerere zandondozana zitanyamula masamba. 2. Njuchi ikuuluka paduwa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Chilengedwe Chimatithandiza Kuti Tizidalira Kwambiri Nzeru za Yehova

Kodi nthawi zonse Yehova amadziwa zinthu zimene zili zabwino kwa ife? Inde. Tikamakhulupirira zimenezi, n’kumatsatira malangizo ake, timasonyeza kuti ndife anzeru. (Miy 16:3, 9) Komabe timakhala pangozi yoti tikhoza kusiya kumudalira ngati malangizo ake akusemphana ndi zimene ife tikuganiza. Tikhoza kumadalira kwambiri nzeru za Yehova tikamaganizira zinthu zimene analenga.​—Miy 30:24, 25; Aro 1:20.

ONERANI VIDIYO YAKUTI KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA? MMENE NYERERE ZIMAPEWERA KUTCHINGIRANA NJIRA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi nyerere zambiri zimagwira ntchito yotani tsiku lililonse?

  • Kodi nyerere zimapewa bwanji kutchingirana njira?

  • Kodi anthu angaphunzirepo chiyani pa mmene nyerere zimayendera?

ONERANI VIDIYO YAKUTI KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA? MMENE NJUCHI IMAULUKIRA, KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kodi anthu amene amayendetsa ndege zing’onozing’ono amakumana ndi mavuto otani?

  • Kodi njuchi zimakwanitsa bwanji kuuluka bwinobwino osakankhidwa ndi mphepo yamphamvu?

  • Kodi anthu m’tsogolomu angadzapindule bwanji potengera nzeru za njuchi?

Kodi kumene mumakhala mwaona umboni wotani wokhudza nzeru za Yehova pa zinthu zimene analenga?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena