KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Zimene Tinganene
Ulendo Woyambaa
Funso: Kodi timadziwa bwanji kuti Mulungu amatiganizira aliyense payekha?
Lemba: Mt 10:29-31
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Mulungu amatithandiza bwanji kuti tizipirira mavuto amene tikukumana nawo?
LEMBALI LIKUPEZEKA MU:
Ulendo Wobwerezab
Funso: Kodi Mulungu amatithandiza bwanji kuti tizipirira mavuto amene tikukumana nawo?
Lemba: Yer 29:11
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Baibulo lingatitsogolere bwanji?
LEMBALI LIKUPEZEKA MU:
lffi 7