Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsamba 12
  • Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Mafunso Ochokera kwa Oŵerenga
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Elisa Anaona Magaleta Oyaka Moto​—Kodi Inunso Mukuwaona?
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Chitsanzo cha Kudzimana ndi Kukhulupirika
    Nsanja ya Olonda—1997
  • Yehova Anagwiritsa Ntchito Akazi Awiri Populumutsa Anthu Ake
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 September tsamba 12
Elisa akuonerera pamene Eliya akugawa madzi a mu mtsinje wa Yorodano ndi chovala chake cha uneneri.

Elisa akuonerera pamene Eliya akupanga chozizwitsa

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Chitsanzo Chabwino cha Kuphunzitsa Ena

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Mafumu.]

Elisa ankaona pamene Eliya ankachita chozizwitsa (2Mf 2:8; w15 4/15 13 ¶15; onani chithunzi chapachikuto)

Modzichepetsa, Elisa anagwiritsa ntchito zomwe anaphunzitsidwa (2Mf 2:13, 14; w15 4/15 13 ¶16)

Mkulu akumvetsera pamene m’bale akuyeserera kukamba nkhani. Mkulu watsegula kabuku ka “Kuphunzitsa.”

Yehova anapereka udindo kwa akulu mumpingo woti aziphunzitsa ena. (2Ti 2:2) Akulu akamakuphunzitsani, muzikhala wofunitsitsa, wodalirika komanso wodzichepetsa.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena