Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 2
  • Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Tikuphunzira pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima Ndiponso Moganizira Ena
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima Ndiponso Moganizira Ena
    Nsanja ya Olonda—2012
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 2
Esitere wakhala payekha, ndipo akuyang’ana mbalame imene ikumwa madzi. Atsikana anzake akudzikongoletsa. Munthu wina akuwayang’anira.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesetsani Kukhala Odzichepetsa Ngati Esitere

[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Esitere.]

Esitere anali mtsikana wokongola kwambiri (Est 2:7)

Esitere anakhalabe wodzichepetsa ngakhale pamene anthu ankamutamanda (Est 2:​9, 15; w17.01 25 ¶11; ia 130 ¶15)

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zolankhula komanso zochita zanga zimasonyeza kuti ndine munthu wotani?’—w17.01 25 ¶12.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena