Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsamba 12
  • Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Timapindula Bwanji ndi Chikondi Chokhulupirika cha Yehova?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2021
  • Kodi Mungatani Kuti Mulungu Akhale Mnzanu?
    Zimene Baibulo Limaphunzitsa
  • Yobu Analemekeza Dzina la Yehova
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Kodi Tingasonyeze Bwanji Kuti Timakonda Yehova?
    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale—Kuphunzira Baibulo Mokambirana
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 September tsamba 12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Chikondi Chokhulupirika cha Mulungu Chimatiteteza ku Mabodza a Satana

Satana amafuna kuti anthu azikhulupirira kuti Yehova ndi amene amachititsa zinthu zoipa (Yob 8:4)

Amafunanso kuti tiziganiza kuti Yehova sizimamukhudza ngati tili okhulupirika kapena ayi (Yob 9:​20-22; w15 7/1 12 ¶3)

Chikondi chokhulupirika cha Yehova chimatithandiza kuti tisamapusitsike ndi mabodza a Satana komanso kuti tikhalabe wokhulupirika (Yob 10:12; Sl 32:​7, 10; w21.11 6 ¶14)

Mlongo akulemba komanso akuganizira madalitso osiyanasiyana amene walandira. Chithunzi chosonyeza banja lina likumupatsa zinthu zimene amugulira, mlongo wina wamuhaga ku Nyumba ya Ufumu, kenako mlongo uja akuonera pulogalamu ya JW Broadcasting.

TAYESANI IZI: Kuti mulimbitse chikhulupiriro chanu, muzifufuza mmene Yehova akukusonyezerani chikondi chokhulupirika, muzilemba zomwe mwapezazo ndipo muziziwerenga mobwerezabwereza.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena