Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • wp24 No. 1 tsamba 16
  • Kodi Malangizo Odalirika Mungawapeze Kuti?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Malangizo Odalirika Mungawapeze Kuti?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2024
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ana Anu Akadzakula Azidzatumikira Mulungu?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2020
  • Zosankha Zimene Zimabweretsa Chisangalalo
    Nsanja ya Olonda—2007
  • Achinyamata, Muzisankha Zochita Mwanzeru
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Kodi Ufulu Wathu Wosankha Tiziugwiritsa Ntchito Bwanji?
    Galamukani!—2003
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2024
wp24 No. 1 tsamba 16
Mnyamata yemwe ali m’nkhani zam’mbuyozi waima pa njira ndipo akuyang’ana pamapu. Patsogolo pake pali polo lokhala ndi zikwangwani zoloza malo osiyanasiyana ndipo chakutsogolo kukuoneka nsonga ya phiri.

Kodi Malangizo Odalirika Mungawapeze Kuti?

Popeza kuti zinthu padzikoli zikusintha kwambiri, kodi n’chiyani chingakuthandizeni kutsimikizira kuti zimene mwasankha kuchita zidzakuthandizani? Kodi mungatsimikizire bwanji kuti zimene mungasankhe lero ndi zabwinodi moti m’tsogolo simungadzadziimbe mlandu kuti munasankha molakwika?

Baibulo lingakuthandizeni kusankha zinthu zimene simungadzanong’onoze nazo bondo. Kodi zimenezi zingatheke bwanji? Baibulo linachokera kwa Mlengi wathu ndipo iye amadziwa bwino zinthu zimene zingatithandize kuti tikhale osangalala komanso kuti tidzakhale ndi tsogolo labwino.

“Iye anakuuza . . . zimene zili zabwino.”—Mika 6:8.

Tiyenera kudalira malangizo othandiza amene amapezeka m’Baibulo. Malangizowa ndi “odalirika nthawi zonse, kuyambira panopa mpaka kalekale.”—Salimo 111:8.

Mungachite bwino kwambiri kufufuza nokha kuti muone mmene Baibulo lingakuthandizireni pamene zinthu zikusintha kwambiri m’dzikoli.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena