Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w24 April tsamba 32
  • Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
  • Nkhani Yofanana
  • Muzisankha Zinthu Mwanzeru Kuti Musataye Madalitso Anu
    Nsanja ya Olonda—2013
  • Yakobo Analandira Madalitso
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
  • Amapasa Amene Anali Osiyana
    Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2024
w24 April tsamba 32

ZOTI NDIPHUNZIRE

Anthu Okonda Yehova Amasankha Zinthu Mwanzeru

Werengani Genesis 25:29-34 kuti muone ngati Esau ndi Yakobo anasankha zinthu mwanzeru.

Fufuzani mozama nkhani yake. Kodi n’chiyani chinachitika poyamba? (Gen. 25:20-28) Nanga n’chiyani chinachitika pambuyo pake?​—Gen. 27:1-46.

Fufuzani mozama mfundo zake. Kodi pa nthawiyo mwana woyamba ankakhala ndi ufulu komanso udindo uti?​—Gen. 18:18, 19; w10 5/1 13.

  • Kodi nthawi zonse kukhala mwana woyamba kunkaphatikizapo kukhala kholo la Mesiya? (w17.12 14-15)

Onani zimene mukuphunzirapo, ndipo muzizitsatira. Mosiyana ndi Esau, n’chifukwa chiyani Yakobo ankaona kuti kukhala mwana woyamba n’kofunika kwambiri? (Aheb. 12:16, 17; w03 10/15 28-29) Kodi Yehova ankawaona bwanji anthu awiriwa, nanga n’chifukwa chiyani? (Mal. 1:2, 3) Kodi Esau ankafunika kuchita chiyani kuti asankhe zinthu mwanzeru?

  • Dzifunseni kuti: ‘Kodi ndingasonyeze bwanji kuti ndimayamikira zinthu zauzimu mlungu uliwonse, mwachitsanzo poonetsetsa kuti tikuchita kulambira kwa pabanja?’

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena