Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yb14 tsamba 2-3
  • Lemba la Chaka cha 2014

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Lemba la Chaka cha 2014
  • Buku Lapachaka la Mboni za Yehova 2014
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ufumu wa Mulungu Uli Mumtima mwa Munthu?
    Nsanja ya Olonda—2011
  • Zimene Zinachitika Yesu Asanayambe Utumiki Wake
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
  • Kodi Ufumu Umene Walamulira kwa Zaka 100 Umakukhudzani Bwanji?
    Nsanja ya Olonda—2014
  • Choonadi Chonena za Ufumu wa Mulungu
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawira)—2020
Onani Zambiri
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova 2014
yb14 tsamba 2-3

Lemba La Chaka Cha 2014

“Ufumu Wanu Ubwere.”​—Mateyu 6:10

Zaka pafupifupi 100 zapitazo, Yehova anaika Yesu pampando wachifumu kumwamba. Kuyambira nthawi imeneyo, atumiki a Mulungu akhala akulengeza mwakhama madalitso amene Ufumu wa Khristu udzabweretse. Zidzakhala zosangalatsa kwambiri Yesu akadzayamba kulamulira dzikoli mwachikondi. Dzikoli lidzakhala Paradaiso ndipo anthu onse adzakhala okondana. Sipadzakhala chiwawa, kumenyana, kudwala, kuvutika komanso imfa.

Posachedwapa, tidzaona zinthu zosangalatsazi zikuchitika. Ufumu wa Mulungu ndi weniweni ndipo ukadzabwera, zinthu zonse zimene Yehova analonjeza zidzachitika. Tizipemphera kuti Ufumuwu ubwere, tiziuza ena za Ufumuwu ndiponso tiziganizira zinthu zonse zimene udzachita.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena