Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • ijwfq nkhani 8
  • Kodi a Mboni za Yehova Amalemekeza Zipembedzo Zina?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi a Mboni za Yehova Amalemekeza Zipembedzo Zina?
  • Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Mumadziwa Zotani Zokhudza a Mboni za Yehova?
    Galamukani!—2016
  • Baibulo Lingakuthandizeni Kukhala Ololera
    Nkhani Zina
  • Kodi Mulidi Ololera?
    Nsanja ya Olonda—2001
  • Kukhala Ololera
    Galamukani!—2015
Onani Zambiri
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri
ijwfq nkhani 8
Munthu akuwerenga Baibulo kumalo ogulitsira mabuku

Kodi a Mboni za Yehova Amalemekeza Zipembedzo Zina?

Timatsatira malangizo a m’Baibulo akuti, “lemekezani anthu [onse]” mosayang’ana chipembedzo chawo. (1 Petulo 2:17) Mwachitsanzo, m’mayiko ena muli a Mboni za Yehova ambirimbiri. Ngakhale zili choncho, sitikakamiza andale kapena anthu opanga malamulo kuti aletse zipembedzo zina kapena ntchito imene zipembedzozo zikuchita. Komanso sitiyesa kukopa akuluakulu a boma kuti aike malamulo okakamiza anthu kuti azitsatira mfundo zathu zokhudza makhalidwe abwino komanso zikhulupiriro zachipembedzo chathu. M’malomwake, timalemekeza zikhulupiriro za anthu ena monga mmene timafunira kuti nawonso azilemekeza zimene timakhulupirira.—Mateyu 7:12.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena