-
Genesis 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Kenako Mulungu anati: “Padziko lapansi pamere udzu, zomera zobereka mbewu ndiponso mitengo yobereka zipatso zokhala ndi nthangala, monga mwa mitundu yake.” Ndipo zinaterodi.
-