-
Genesis 4:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Dzina la mʼbale wake wa Yabala linali Yubala. Yubala anali munthu woyamba pa anthu onse oimba zeze ndi chitoliro.
-