-
Genesis 34:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Tikatero, kodi katundu wawo, chuma chawo ndi ziweto zawo zonse sizidzakhala zathu? Ndiye tiyeni tilolere zimene akufunazo kuti azikhala nafe.”
-