Genesis 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pa tsiku lachitatu, anthuwo akumvabe ululu, ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi, alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake nʼkukalowa mumzindawo anthuwo asakuyembekezera ndipo anapha mwamuna aliyense.+
25 Koma pa tsiku lachitatu, anthuwo akumvabe ululu, ana awiri a Yakobo, Simiyoni ndi Levi, alongo ake a Dina,+ aliyense anatenga lupanga lake nʼkukalowa mumzindawo anthuwo asakuyembekezera ndipo anapha mwamuna aliyense.+