-
Genesis 4:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Komanso Zila anabereka Tubala-kaini, amene anali mmisiri wosula zipangizo zamtundu uliwonse zakopa ndi zachitsulo. Ndipo mlongo wake wa Tubala-kaini anali Naama.
-