Genesis 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu.
2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a mʼbanja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu.