Genesis 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho anthuwo anapereka kwa Yakobo milungu yachilendo yonse imene anali nayo, ndi ndolo zimene anavala mʼmakutu. Kenako Yakobo anakwirira* zinthuzo pansi pa mtengo waukulu umene unali pafupi ndi ku Sekemu.
4 Choncho anthuwo anapereka kwa Yakobo milungu yachilendo yonse imene anali nayo, ndi ndolo zimene anavala mʼmakutu. Kenako Yakobo anakwirira* zinthuzo pansi pa mtengo waukulu umene unali pafupi ndi ku Sekemu.