Genesis 35:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake Debora,+ mlezi* wa Rabeka anamwalira, ndipo anamuika ku Beteli mʼmunsi mwa phiri, pansi pa mtengo waukulu. Choncho mtengowo anautchula kuti Aloni-bakuti.*
8 Pambuyo pake Debora,+ mlezi* wa Rabeka anamwalira, ndipo anamuika ku Beteli mʼmunsi mwa phiri, pansi pa mtengo waukulu. Choncho mtengowo anautchula kuti Aloni-bakuti.*