-
Genesis 35:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako anachoka ku Beteliko. Kutatsala mtunda wautali kuti afike ku Efurata, nthawi yoti Rakele abereke inakwana, koma poberekapo anavutika kwambiri.
-