Genesis 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Rakele anamwalira, ndipo anamuika mʼmanda mʼmbali mwa njira yopita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+
19 Choncho Rakele anamwalira, ndipo anamuika mʼmanda mʼmbali mwa njira yopita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+