Genesis 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamapeto pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ mʼdera la Kiriyati-ariba, komwe ndi ku Heburoni. Uku nʼkumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+
27 Pamapeto pake Yakobo anafika kwa bambo ake Isaki ku Mamure,+ mʼdera la Kiriyati-ariba, komwe ndi ku Heburoni. Uku nʼkumenenso Abulahamu ndi Isaki anakhalako monga alendo.+