Genesis 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Adamu anagonanso ndi mkazi wake Hava ndipo anabereka mwana wamwamuna. Hava anapatsa mwanayo dzina lakuti Seti*+ chifukwa atabadwa, Havayo ananena kuti: “Mulungu wandipatsa* mwana wina mʼmalo mwa Abele amene Kaini anamupha.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:25 Nsanja ya Olonda,2/1/2009, tsa. 13
25 Adamu anagonanso ndi mkazi wake Hava ndipo anabereka mwana wamwamuna. Hava anapatsa mwanayo dzina lakuti Seti*+ chifukwa atabadwa, Havayo ananena kuti: “Mulungu wandipatsa* mwana wina mʼmalo mwa Abele amene Kaini anamupha.”+