Genesis 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Imeneyi ndi mibadwo ya Esau, kholo la Aedomu, amene ankakhala kudera lamapiri la Seiri.+